8 Ndipo ana a Yuda anacita nkhondo pa Yerusalemu, naulanda, naukantha ndi lupanga lakuthwa, natentha mudzi ndi moto.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:8 nkhani