17 Ndipo ana a Amoni analalikiridwa, namanga misasa m'Gileadi. Ndi ana a Israyeli anasonkhana namanga misasa ku Mizipa.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 10
Onani Oweruza 10:17 nkhani