Oweruza 11:16 BL92

16 pakuti pakukwera iwo kucokera ku Aigupto Israyeli anayenda m'cipululu mpaka Nyanja Yofiira, nafika ku Kadesi;

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:16 nkhani