Oweruza 11:39 BL92

39 Ndipo kunali pakutha miyezi iwiri, anabwerera kwa atate wace amene anamcitira monga mwa cowinda cace anaciwinda; ndipo sanamdziwa mwamuna. Motero unali mwambo m'Israyeli,

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:39 nkhani