Oweruza 12:1 BL92

1 Pamenepo amuna a Efraimu analalikidwa, napita kumpoto; nati kwa Yefita, Wapitiriraoji kuthira nkhondo ana a Amoni, osatiitana ife timuke nawe? Tidzakutenthera nyumba yako ndimotopamtupako.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 12

Onani Oweruza 12:1 nkhani