11 Nanyamuka Manowa natsata mkazi wace, namdzera mwamuna uja, nanena naye, Kodi ndinu mwamuna ujamunalankhulandimkaziyu? Ndipo anati, Ndine amene.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 13
Onani Oweruza 13:11 nkhani