17 Ndipo Manowa anati kwa mthenga wa Yehova, Dzina lanu ndani, kuti, atacitika mau anu, tikucitireni ulemu.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 13
Onani Oweruza 13:17 nkhani