Oweruza 13:19 BL92

19 Pamenepo Manowa anatenga mwana wa mbuzi pamodzi ndi nsembe yaufa, nazipereka kwa Yehova pathanthwe; ndipo mthengayo anacita modabwitsa, ndi Manowa ndi mkazi wace ali cipenyereo

Werengani mutu wathunthu Oweruza 13

Onani Oweruza 13:19 nkhani