Oweruza 13:21 BL92

21 Ndipo mthenga wa Yehova sanaonekeranso kwa Manowa kapena kwa mkazi wace. Pamenepo anadziwa Manowa kuti ndiye mthenga wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 13

Onani Oweruza 13:21 nkhani