Oweruza 13:23 BL92

23 Koma mkazi wace ananena naye, Yehova akadafuna kutipha, sakadalandira nsembe yopsereza ndi nsembe yaufa pa dzanja lathu, kapena kutionetsa izi zonse, kapena kutimvetsa zoterezi nthawi yino.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 13

Onani Oweruza 13:23 nkhani