Oweruza 14:15 BL92

15 Koma kunali, tsiku lacisanu ndi ciwiri anati kwa mkazi wa Samsoni, Kopa mwamuna wako, atitanthauzire mwambiwo; tingatenthe iwe ndi nyumba ya atate wako ndi mota. Kodi mwatiitana kulanda zathu; si momwemo?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:15 nkhani