Oweruza 14:9 BL92

9 Ndipo anaufula ndi dzanja lace, nayenda, namadya alimkuyenda, nadza kwa atate wace ndi amai wace, nawapatsa, nadya iwo; koma sanawauza kuti adaufula uciwo m'citanda ca mkango.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:9 nkhani