Oweruza 15:1 BL92

1 Ndipo kunali atapita masiku, nyengo ya kuceka tirigu Samsoni anakaceza ndi mkazi wace ndi kumtengera mbuzi, nati, Ndidzalowa kwa mkazi wanga kucipinda. Koma atate wace sanamlola kulowamo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:1 nkhani