Oweruza 15:11 BL92

11 Pamenepo anatsikira ku phanga la Etamu amuna zikwi zitatu, nati kwa Samsoni, Sudziwa kodi kuti Atilisti ndiwo akutilamulira ife? nciani ici waticitira? Nati iye kwa iwowa, Monga anandicitira ine ndawacitira iwo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:11 nkhani