Oweruza 15:18 BL92

18 Ndipo anamva ludzu lambiri, naitana kwa Yehova, nati, Mwapatsa Inu cipulumutso ici cacikuru ndi dzanja la kapolo wanu; ndipo kodi ndife nalo ludzu tsopano ndi kugwa m'dzanja la osadulidwa awa?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:18 nkhani