Oweruza 15:4 BL92

4 Namuka Samsoni, nagwira ankhandwe mazana atatu, natenga miuni, nalunza micira, naika muuni pakati pa micira iwiri iri yonse.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:4 nkhani