Oweruza 15:6 BL92

6 Pamenepo Afilisti anati, Wacita ici ndani? Nati, Samsoni mkamwini wa munthuyo wa ku Timna, popeza analanda mkazi wace, nampereka kwa mnzace. Pamenepo Afilisti anakwera namtentha mkaziyo ndi atate wace ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 15

Onani Oweruza 15:6 nkhani