Oweruza 16:13 BL92

13 Pamenepo Delila anati kwa Samsoni, Mpaka tsopano wandipusitsa, ndi kundiuza mabodza; undiuze cimene angakumange naco. Nanena naye, Ukaomba njombi zisanu ndi ziwiri za pamutu panga mwa thonje loyala ndiko.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:13 nkhani