Oweruza 16:15 BL92

15 Pamenepo ananena naye, Ukati bwanji, Ndikukonda, osamvana nane mtima wako? wandipusitsa katatu tsopano, osandiuza umo mucokera mphamvu yako yaikuru,

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:15 nkhani