5 Ndipo akalonga a Atilisti anamkwerera mkaziyo, nanena naye, Umkope nuone umo mucokera mphamvu yace yaikuru, ndi umo tingakhoze kumtha khama, kuti timmange kumzunza; ndipo tidzakupatsa ali yense ndalama mazana khumi ndi limodzi.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 16
Onani Oweruza 16:5 nkhani