Oweruza 17:2 BL92

2 Ndipo iye anati kwa amai wace, Ndarama zija mazana khumi ndi limodzi anakuberani zimene munatembererapo, ndi kunenanso m'makutu mwanga, taonani ndaramazo ndiri nazo, ndinazitenga ndine. Pamenepo amai wace anati, Yehova adalitse mwana wanga.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 17

Onani Oweruza 17:2 nkhani