Oweruza 18:1 BL92

1 Masiku ajawo panalibe mfumu m'Israyeli; masiku ajanso pfuko la Adani anadzifunira colowa cakukhalako; pakuti kufikira tsiku lija sicinawagwera colowa cao pakati pa mapfuko a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:1 nkhani