Oweruza 18:12 BL92

12 Nakwera namanga misasa m'Kiriyati-yearimu, m'Yuda; cifukwa cace anacha dzina lace la malowo cigono ca Dani, mpaka lero; taona, ali m'tseri mwa Kiriyatiyearimu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:12 nkhani