Oweruza 18:27 BL92

27 M'mwemo anatenga zimene Mika adacipanga, ndi wansembe anali naye, nafika ku Laisi, kwa anthu odekha ndi okhazikika mtima, nawakantha ndi lupanga lakuthwa, natentha mudzi wao ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:27 nkhani