Oweruza 18:30 BL92

30 Ndipo ana a Dani anadziimitsira fane losemalo; ndi Yonatani mwana wa Gerisomu mwana wa Manase, iye ndi ana ace amuna anali ansembe a pfuko la Adani mpaka tsiku lija anatenga ndende anthu a m'dziko.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 18

Onani Oweruza 18:30 nkhani