Oweruza 19:19 BL92

19 Ngakhale maudzu ndi cakudya ca aburu athu ziriko; ndi mkate ndi vinyo zirikonso kwa ine ndi kwa mdzakazi wako ndi kwa mnyamata wokhala ndi aka polo ako; kosasowa kanthu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:19 nkhani