Oweruza 19:21 BL92

21 Pamenepo anamlonga m'nyumba yace, napatsa aburu cakudya; ndipo iwo anasamba mapazi ao, nadya, namwa.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 19

Onani Oweruza 19:21 nkhani