Oweruza 2:12 BL92

12 nasiya Yehova Mulungu wa makolo ao, amene adawaturutsa m'dziko la Aigupto, natsata milungu yina, milungu ya mitundu ya anthu okhala pozungulira pao, naigwadira; nautsa mkwiyo wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 2

Onani Oweruza 2:12 nkhani