17 Koma sanamvera angakhale oweruza ao, pakuti anamuka kupembedza milungu yina, naigwadira; anapambuka msanga m'njira yoyendamo makolo ao, pomvera malamulo a Yehova; sanatero iwowa.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 2
Onani Oweruza 2:17 nkhani