Oweruza 2:19 BL92

19 Koma kunali atafa woweruzayo anabwerera m'mbuyo, naposa makolo ao ndi kucita moipitsa, ndi kutsata milungu yina kuitumikira ndi kuigwadira, sanaleka kanthu ka macitidwe ao kapena ka njira yao yacheni.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 2

Onani Oweruza 2:19 nkhani