Oweruza 2:2 BL92

2 ndipo inu, musamacita pangano ndi nzika za m'dziko ili; muzigamula maguwa ao a nsembe. Koma simunamvera mau anga; mwacicita ici cifukwa ninji?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 2

Onani Oweruza 2:2 nkhani