Oweruza 2:7 BL92

7 Ndipo anthuwo anatumikira Yehova masiku onse a Yoswa ndi masiku onse a akulu akulu otsala atafa Yoswa, amene adaona nchito yaikuru yonse ya Yehova anaicitira Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 2

Onani Oweruza 2:7 nkhani