Oweruza 20:32 BL92

32 Ndipo ana a Benjamini anati, Tawakantha pamaso pathu monga poyamba paja. Koma ana a Israyeli anati, Tithawe, tiwakokere kutari ndi mudzi kumakwalala.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:32 nkhani