Oweruza 20:42 BL92

42 Nabwerera iwo pamaso pa amuna a Israyeli kumka njira ya cipululu; koma nkhondo inawaloodetsa; ndi aja oturuka m'mudzi anawaononga pakati pao.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:42 nkhani