Oweruza 20:45 BL92

45 Natembenuka iwo, nathawira kucipululu ku thanthwe la Rimoni; koma anawakunkha m'makwalala amuna zikwi zisanu; nawalondetsa ku Gidomu, nakantha a iwowa amuna zikwi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:45 nkhani