Oweruza 20:48 BL92

48 Ndipo amuna a Israyeli anabwereranso kwa ana a Benjamini, nawakantha ndi lupanga lakuthwa a m'mudzi wonse, ndi zoweta, ndi zonse adazipeza; anatenthanso midzi yonse anaipeza.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 20

Onani Oweruza 20:48 nkhani