Oweruza 21:10 BL92

10 Ndipo msonkhano unatumizako amuna zikwi khumi ndi ziwiri, ndiwo ngwazi, nawalamulira ndi kuti, Mukani, nimuwakanthe okhala m'Yabesi-gileadi ndi lupanga lakuthwa, ndi akazi ndi ana ang'ono.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 21

Onani Oweruza 21:10 nkhani