12 Ndipo anapeza mwa anthu a Yabesi-gileadi anamwali mazana anai osadziwa mwamuna mogona naye; nabwera nao kumisasa ku Silo, ndiwo a m'dziko la Kanani.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 21
Onani Oweruza 21:12 nkhani