Oweruza 21:19 BL92

19 Natiiwo, Taonani, pali madyerero a Yehova caka ndi caka ku Silo, ndiko kumpoto kwa Beteli, kum'mawa kwa mseu wokwera kucokera ku Beteli kumka ku Sekemu, ndi kumwela kwa Lebona.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 21

Onani Oweruza 21:19 nkhani