2 Ndipo anthu anadza ku Beteli, nakhala pansi pomwepo pamaso pa Mulungu mpaka madzulo; nakweza mau ao ndi kulira misozi yambiri.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 21
Onani Oweruza 21:2 nkhani