Oweruza 3:16 BL92

16 Ndipo Ehudi anadzisulira lupanga lakuthwa konse konse utali wace mkono; nalimangirira pansi pa zobvala zace pa ncafu ya kulamanja.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 3

Onani Oweruza 3:16 nkhani