22 ndi cigumbu cace cinalowa kutsata mpeni wace; ndi mafuta anaphimba mpeniwo, pakuti sanasolola lupanga m'mimba mwace; nilituruka kumbuyo.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 3
Onani Oweruza 3:22 nkhani