24 Ndipo ataturuka iye, anadza aka polo ace; napenya, ndipo taonani pamakomo pa cipinda cosanja mpofungulira; nati iwo, Angophimba mapazi m'cipinda cace cosanja copitidwa mphepo.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 3
Onani Oweruza 3:24 nkhani