Oweruza 3:3 BL92

3 anasiya mafumu asanu a Afilisti ndi Akanani onse, ndi Asidoni, ndi Ahivi okhala m'phiri la Lebano, kuyambira phiri la Baalaherimoni mpaka polowera ku Hamati.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 3

Onani Oweruza 3:3 nkhani