31 Atapita iye kunali Samagara, mwana wa Anati amene anakantha Afilisti mazana asanu ndi limodzi ndi mtoso wa ng'ombe; nayenso anapulumutsa Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 3
Onani Oweruza 3:31 nkhani