Oweruza 4:11 BL92

11 Ndipo Heberi Mkeni anadzisiyanitsa ndi Akeni, ndi ana a Hobabu mlamu wace wa Mose, namanga mahema ace mpaka thundu wa m'Zaananimu, ndiwo wa ku Kedesi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 4

Onani Oweruza 4:11 nkhani