Oweruza 4:13 BL92

13 Pamenepo Sisera anasonkhanitsa magareta ace onse ndiwo magareta mazana asanu ndi anai acitsulo, ndi anthu onse okhala naye, kuyambira Haroseti wa amitundu mpaka mtsinje wa Kisoni.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 4

Onani Oweruza 4:13 nkhani