Oweruza 4:22 BL92

22 Ndipo taonani, pomlondola Sisera Barakiyo, Yaeli anaturuka kukomana naye, Dati kwa iye, Idza kuno, ndidzakuonetsa munthu umfunayo, Potero anamdzera, ndipo taonani, Sisera wagwa, wafa, ndi ciciri m'litsipa mwace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 4

Onani Oweruza 4:22 nkhani