24 Ndipo dzanja la ana a Israyeli linamkabe ndi kulimbika pa Yabini mfumu ya Kanani mpaka adamuononga Yabini mfumu ya Kanani.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 4
Onani Oweruza 4:24 nkhani