Oweruza 4:9 BL92

9 Nati iye, Kumuka ndidzamuka nawe, koma ulendo umukawo, sudzacita nao ulemu; pakuti: Yehova adzagulitsa Sisera m'dzanja la mkazi, Motero Debora anauka namuka ndi Baraki ku Kedesi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 4

Onani Oweruza 4:9 nkhani